Mwata, Chasefu
Mwata ni msumba mu Boma la Chasefu, Zambia.
Ndyali
lembaMsumba uli ndi likulu, lomwe lingagwiritsidwe ntchito polembetsa ovota ku Chasefu Town Council pa zisankho za ECZ, matauni awa ndi Boyole, Chasefu, Malandula, Mthwalo, Chambuzi, Mbenje, Khulamayembe, Mwata, Zozo, Kaponga, Lusuntha, Phikamalaza, Kamzoole, Kakoma, Khufyu, Kamusis, na Hoya. [1]